
Kabambe alandiridwa mwachikondi ku Mulanje Bale
Olemba Burnett Munthali Lero pa Lachinayi, 1 May 2025, anthu a ku Mulanje Bale anasonkhana ndi chimwemwe chachikulu polandiridwa Purezidenti wa Chipani cha UTM, Dr. Dalitso Kabambe. Linali tsiku lodzaza ndi chisangalalo, mgwirizano, komanso chiyembekezo …